2 Samueli 19:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco mfumu inabwera nifika ku Yordano. Ndipo Ayuda anadza ku Giligala, kuti akakomane ndi mfumu, ndi kumuolotsa mfumu pa Yordano.

2 Samueli 19

2 Samueli 19:10-19