2 Samueli 19:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo anauza Yoabu, Onani mfumu irikulira misozi, nilira Abisalomu.

2. Ndipo cipulumutso ca tsiku lila cinasandulika maliro kwa anthu onse; pakuti anthu anamva kuti, Mfumu iri ndi cisoni cifukwa ca mwana wace.

2 Samueli 19