2 Samueli 18:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco anthuwo anaturukira kuthengo kukamenyana ndi Israyeli; nalimbana ku nkhalango ya ku Efraimu.

2 Samueli 18

2 Samueli 18:1-16