2 Samueli 18:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inati, Kodi mnyamatayo Abisalomu ali bwino? Ahimaazi nayankha, Pamene Yoabu anatumiza mnyamata wa mfumu, ndiye ine mnyamata wanu, ndinaona piringu piringu, koma sindinadziwa ngati kutani.

2 Samueli 18

2 Samueli 18:22-33