2 Samueli 18:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoabu ananena naye, Sudzakhala iwe wotengera mau lero, koma tsiku lina udzatengera mau; koma lero sudzatengera mau, cifukwa mwana wa mfumu wafa.

2 Samueli 18

2 Samueli 18:16-21