2 Samueli 18:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatenga Abisalomu namponya m'cidzenje cacikuru kunkhalangoko; naunjika pamwamba pace mulu waukuru ndithu wamiyala; ndipo Aisrayeli onse anathawa yense ku hema wace.

2 Samueli 18

2 Samueli 18:12-19