2 Samueli 17:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali pakufika Davide ku Mahanaimu, Sobi mwana wa Nahasi wa ku Raba wa ana a Amoni, ndi Makiri mwana wa Amiyeli wa ku Lodebara, ndi Barizilai Mgileadi wa ku Rogelimu,

2 Samueli 17

2 Samueli 17:25-29