2 Samueli 17:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngakhale ngwazi imene mtima wace ukunga mtima wa mkango idzasungunuka konse, pakuti Aisrayeli onse adziwa atate wanu kuti ndiye munthu wamphamvu, ndi iwo ali naye ndiwo ngwazi.

2 Samueli 17

2 Samueli 17:9-18