2 Samueli 16:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakufika mfumu Davide ku Bahurimu, onani, panaturuka pamenepo munthu wa banja la nyumba ya Sauli, dzina lace ndiye Simeyi, mwana wa Gera; iyeyu anaturukako, nayenda natukwana.

2 Samueli 16

2 Samueli 16:1-12