2 Samueli 16:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inati, Mwana wa mbuye wako ali kuti? Ziba nanena ndi mfumu, Onani, akhala ku Yerusalemu; pakuti anati, Lero nyumba ya Israyeli idzandibwezera ufumu wa atate wanga.

2 Samueli 16

2 Samueli 16:2-8