2 Samueli 16:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uphungu wa Ahitofeli anaupangira masiku aja, unali monga ngati munthu anafunsira mau kwa Mulungu; uphungu wonse wa Ahitofeli unali wotere kwa Davide ndi kwa Abisalomu yemwe.

2 Samueli 16

2 Samueli 16:18-23