2 Samueli 15:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inanenanso ndi Zadoki wansembeyo, Suli mlauli kodi? ubwere kumudzi mumtendere pamodzi ndi ana ako amuna awiri, Ahimaazi mwana wako ndi Jonatani mwana wa Abyatara.

2 Samueli 15

2 Samueli 15:25-29