2 Samueli 15:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Itai nayankha mfumu nuti, Pali Yehova, pali mbuye wanga mfumu, zoonadi apo padzakhala mbuye wanga mfumu, kapena mpa imfa kapena mpa moyo, pomwepo padzakhalanso mnyamata wanu.

2 Samueli 15

2 Samueli 15:20-26