2 Samueli 14:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mdzakazi wanu ndinali nao ana amuna awiri, ndipo awiriwa analimbana kumunda, panaboo wina wakuwaletsa, koma wina anakantha mnzace namupha.

2 Samueli 14

2 Samueli 14:1-8