2 Samueli 14:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene mkazi wa ku Tekowayo anati alankhule ndi mfumuyo, anagwa nkhope yace pansi namlambira, nati, Ndithandizeni mfumu.

2 Samueli 14

2 Samueli 14:1-9