2 Samueli 14:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kwa Abisalomu kunabadwa ana amuna atatu ndi mwana wamkazi mmodzi, dzina lace ndiye Tamara, iye ndiye mkazi wokongola nkhope.

2 Samueli 14

2 Samueli 14:25-29