2 Samueli 14:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mnyamata wanu Yoabu anacita cinthu ici kuti asandulize mamvekedwe a mranduwo. Ndipo mbuye wanga ali wanzeru, monga ndi nzeru ya mthenga wa Mulungu, kudziwa zonse ziri m'dziko lapansi.

2 Samueli 14

2 Samueli 14:16-24