2 Samueli 14:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoabu anatumiza ku Tekowa, natenga kumeneko mkazi wanzeru, nanena naye, Ukokomezeke monga mfedwa, nubvale zobvala za pamaliro, osadzola mafuta, koma ukhale ngati munthu wamkazi wakulira akufa nthawi yaikuru.

2 Samueli 14

2 Samueli 14:1-3