2 Samueli 14:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu inayankha, ninena naye mkaziyo, Usandibisire kanthu ka zimene ndidzakufunsa iwe. Mkaziyo nati, Mbuye wanga mfumu anene.

2 Samueli 14

2 Samueli 14:16-23