2 Samueli 14:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tsono cakuti ndadzanena mau awa ndi mbuye wanga mfumu, ndico kuti anthu anandiopsa ine; ndipo mdzakazi wanu ndinati, Ndilankhuletu ndi mfumu; kapena mfumu idzacita copempha mdzakazi wace.

2 Samueli 14

2 Samueli 14:8-17