2 Samueli 14:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Mfumu mukumbukile Yehova Mulungu wanu kuti wolipsa mwazi asaonjeze kuononga, kuti angaononge mwana wanga. Niti iyo, Pali Yehova, palibe tsitsi limodzi la mwana wako lidzagwa pansi.

2 Samueli 14

2 Samueli 14:1-13