2 Samueli 13:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanena naye, Iwe mwana wa mfumu, uonderanji tsiku ndi tsiku? Sungandiuze kodi? Ndipo Amnoni anati kwa iye, Ndikonda Tamara, mlongo wa mbale wanga Abisalomu.

2 Samueli 13

2 Samueli 13:3-8