2 Samueli 13:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu inanyamuka ning'amba zobvala zace nigona pansi, ndipo anyamata ace onse anaimirirapo ndi zobvala zao zong'ambika.

2 Samueli 13

2 Samueli 13:21-39