2 Samueli 13:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zitapita zaka ziwiri zathunthu, kunali kuti Abisalomu anali: nao osenga nkhosa zace ku Baalahazore pafupi pa Efraimu; ndipo Abisalomu anaitana ana amuna onse a mfumu.

2 Samueli 13

2 Samueli 13:17-29