2 Samueli 12:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene Davide anaona anyamata ace alikunong'onezana, Davide anazindikira kuti mwanayo adafa; Davide nanena ndi anyamata ace, Kodi mwanayo wafa? Nati iwo, Wafa.

2 Samueli 12

2 Samueli 12:16-25