2 Samueli 11:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anauza Uriya, Utsikire ku nyumba yako, nutsuke mapazi ako, Ndipo Uriya anacoka ku nyumba ya mfumu, ndipo anamtsata munthu ndi mphatso ya mfumu.

2 Samueli 11

2 Samueli 11:7-11