2 Samueli 11:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakuturuka malirowo, Davide anatumiza munthu namtenga afike kwao ku nyumba yace; ndipo iyeyo anakhala mkazi wace nambalira mwana wamwamuna. Koma Yehova anaipidwa ndi cinthu cimene Davide adacita.

2 Samueli 11

2 Samueli 11:17-27