2 Samueli 11:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akuponyawo amene anali palinga anaponya anyamata anu; ndipo anyamata ena a mfumu anafa, ndi mnyamata wanu Uriya Mhiti, iyenso anafa.

2 Samueli 11

2 Samueli 11:22-26