2 Samueli 11:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali pa madzulo Davide anauka pa kama wace nayenda pa tsindwi la nyumba ya mfumu. Ndipo iye ali patsindwipo anaona mkazi alinkusamba; ndi mkaziyo anali wocititsa kaso pomuyang'ana.

2 Samueli 11

2 Samueli 11:1-5