2 Samueli 11:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akumudziwo anaturuka, namenyana ndi Yoabu; ndipo adagwapo anthu ena, ndiwo a anyamata a Davide; ndi Uriya Mhiti anafanso.

2 Samueli 11

2 Samueli 11:15-27