2 Samueli 11:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakumuitana Davide, iyeyo anadya namwa pamaso pace; Davide namledzeretsa; ndipo usiku anaturuka kukagona pa kama wace pamodzi ndi anyamata a mbuye wace; koma sanatsildra ku nyumba yace.

2 Samueli 11

2 Samueli 11:4-20