2 Samueli 10:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Amoni anaturuka, nandandalitsa nkhondo polowera kucipata. Ndipo Aaramu a ku Zoba ndi a ku Rehobu, ndi anthu a Tobu ndi Maaka, anali pa okha kuthengo.

2 Samueli 10

2 Samueli 10:1-9