2 Samueli 10:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hadarezeri anatumiza mthenga nakatenga Aaramu a ku tsidya la cimtsinje; iwo nafika ku Helamu, ndi Sobaki kazembe wa khamu la nkhondo la Hadarezeri anawatsogolera.

2 Samueli 10

2 Samueli 10:15-19