2 Samueli 10:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anati, Aaramu akandipambana ine, udzandithandiza ndiwe, koma ana a Amoni akapambana iwe, tsono ndidzabwera ine kukuthandiza.

2 Samueli 10

2 Samueli 10:3-18