2 Samueli 1:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma asanafe, Davide adanena naye, Wadziphetsa ndi mtima wako; cifukwa pakamwa pako padacita umboni wakukutsutsa ndi kuti, Ine ndinapha wodzozedwa wa Yehova.

2 Samueli 1

2 Samueli 1:14-22