2 Petro 3:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akuyembekezera ndi kufulumira kwa kudza kwace kwa tsiku la Mulungu, m'menemo miyamba potentha mota idzakanganuka, ndi zam'mwamba zidzasungunuka ndi kutentha kwakukuru.

2 Petro 3

2 Petro 3:6-18