2 Petro 2:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo sanalekerera dziko lapansi lakale, koma anasunga Nowa mlaliki wa cilungamo, ndi anzace asanu ndi awiri, pakulitengera dziko la osapembedza cigumula;

2 Petro 2

2 Petro 2:1-9