2 Petro 2:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ngati, adatha kuthawa zodetsa za dziko lapansi mwa cizindikiritsoca, Ambuye ndi Mpulumutsi Yesu Kristu, akodwanso nazo, nagonjetsedwa, zorsiriza zao zidzaipa koposa zoyambazo,

2 Petro 2

2 Petro 2:10-22