2 Petro 2:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma awo, ngati zamoyo zopanda nzeru, nyama zobadwa kuti zikodwe ndi kuonongedwa, akucitira mwano pa zinthu osazidziwa, adzaonongeka m'kuononga kwao,

2 Petro 2

2 Petro 2:4-14