2 Petro 1:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mwa izi adatipatsa malonjezano a mtengo wace ndi akuru ndithu; kuti mwa izi mukakhale oyanjana nao umulungu wace, mutapulumuka ku cibvundi ciri pa dziko lapansi m'cilakolako.

2 Petro 1

2 Petro 1:1-8