2 Petro 1:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti sitinatsata miyambi yacabe, pamene tinakudziwitsani mphamvu ndi maonekedwe a Ambuye wathu Yesu Kristu, koma tinapenya m'maso ukulu wace.

2 Petro 1

2 Petro 1:7-21