2 Mbiri 9:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkaziyo anapatsa mfumu matalente a golidi zana limodzi mphambu makumi awiri, ndi zonunkhira zambiri ndithu, ndi timiyala ta mtengo wace; panalibe zonunkhira zina zonga zija mfumu yaikazi ya ku Seba anapatsa mfumu Solomo.

2 Mbiri 9

2 Mbiri 9:1-10