2 Mbiri 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma sindinakhulupira mau ao mpaka ndinadza, ndaona ndi maso anga; ndipo taonani anandifotokozera dera lina lokha la nzeru zanu zocuruka; mwa, onjezatu pa mbiri ndidaimva.

2 Mbiri 9

2 Mbiri 9:1-8