2 Mbiri 9:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Macitidwe ena tsono a Solomo, oyamba ndi otsiriza, salembedwa kodi m'buku la mau a Natani mneneri ndi m'zonenera za Ahiya wa ku Silo, ndi m'masomphenya a Ido mlauli za Yerobiamu mwana wa Nebati?

2 Mbiri 9

2 Mbiri 9:23-31