2 Mbiri 9:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kulemera kwace tsono kwa golidi anafika kwa Solomo caka cimodzi ndiko matalente mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi kudza asanu ndi limodzi a golidi;

2 Mbiri 9

2 Mbiri 9:3-23