2 Mbiri 8:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo anamkweretsa mwana wamkazi wa Farao m'mudzi wa Davide, alowe m'nyumba imene adammangira; pakuti anati, Mkazi wanga asakhale m'nyumba ya Davide mfumu ya Israyeli; popeza mpopatulika pamene panafika likasa la Yehova.

2 Mbiri 8

2 Mbiri 8:2-12