2 Mbiri 7:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nthawi yomweyo Solomo anacita madyerero masiku asanu ndi awiri, ndi Aisrayeli onse pamodzi naye, khamu lalikuru ndithu, kuyambira polowera ku Hamati kufikira mtsinje wa ku Aigupto.

2 Mbiri 7

2 Mbiri 7:3-18