2 Mbiri 7:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Solomo anapereka nsembe ya ng'ombe zikwi makumi awiri mphambu ziwiri, ndi nkhosa zikwi, makumi awiri. Momwemo mfumu ndi anthu onse anapereka nyumba ya Yehova.

2 Mbiri 7

2 Mbiri 7:1-11