2 Mbiri 7:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzayankha, Popeza anasiya Yehova Mulungu wa makolo ao amene anawaturutsa m'dziko la Aigupto, nagwira milungu yina, nailambira ndi kuitumikira; cifukwa cace anawagwetsera coipa ici conse.

2 Mbiri 7

2 Mbiri 7:17-22