2 Mbiri 7:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo ndidzawazula m'dziko langa limene ndinawapatsa; ndi nyumba yino ndinaipatulira dzina langa ndidzaitaya, osaionanso, ndi kuiyesa mwambi ndi mnyozo mwa mitundu yonse ya anthu.

2 Mbiri 7

2 Mbiri 7:18-22